Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye anali ndi mwana wamwamuna dzina lace Sauli, mnyamata wokongola; pakati pa anthu onse a Israyeli panalibe wina wokongola ngati iye; anali wamtali, anthu onse ena anamlekeza m'cifuwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:2 nkhani