Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mutafika m'mudzi, pomwepo mudzampeza, asanakwere kumsanje kukadya; pakuti anthu sadzadya, koma iye atafika ndipo; pakuti iye amadalitsa nsembeyo; ndipo atatero oitanidwawo amadya. Cifukwa cace kwerani; popeza nthawi yino mudzampeza.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:13 nkhani