Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa, nampereka wathunthu kwa Yehova, nsembe yopsereza; ndipo Samueli anapempherera Israyeli kwa Yehova; ndipo Yehova anambvomereza.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7

Onani 1 Samueli 7:9 nkhani