Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 7:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Samueli analikupereka nsembe yopserezayo, Afilisti anayandikira kuti aponyane ndi Aisrayeli; koma tsiku lomwe lija Yehova anagunda ndi kugunda kwakukuru pa Afilistiwo, nawapolonganitsa. Ndipo anakanthidwa pamaso pa Aisrayeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7

Onani 1 Samueli 7:10 nkhani