Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muyang'anire, ngati likwera pa njira ya malire ace ace ku Betisemesi, iye anaticitira coipa ici cacikuru; koma likapanda kutero, tidzadziwapo kuti dzanja limene linatikantha, siliri lace; langotigwera tsokali.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:9 nkhani