Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 6:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulikuumitsiranji mitima yanu, monga Aaigupto ndi Farao anaumitsa mitima yao? Kodi iwo sana lola anthuwo amuke, iye atacita kodabwitsa pakati pao, ndipo anamuka?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:6 nkhani