Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiponso mbewa zagolidi, monga ciwerengo ca midzi yonse ya mafumu asanu a Afilisti, midzi ya malinga, ndi midzi ya kumiraga; kufikira ku mwala waukuru, adaikapo likasa la Yehova; mwalawo ulipobe kufikira lero m'munda wa Yoswa wa ku Betisemesi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6

Onani 1 Samueli 6:18 nkhani