Ndipo amenewa ndiwo mafundo agolidi amene anabwezera kwa Yehova akhale nsembe yoparamula, kwa Asidodi limodzi, kwa Gaza limodzi, kwa Asikeloni limodzi, kwa Gati limodzi, kwa Ekroni limodzi;