Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace anatumiza likasa la Mulungu ku Ekroni. Ndipo kunali pofika likasalo ku Ekroni, a ku Ekroni anapfuula nati, Anadzatitulira likasa la Mulungu wa Israyeli, kutipha ife ndi ana athu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 5

Onani 1 Samueli 5:10 nkhani