Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace anatumiza ku Silo kuti akatenge kumeneko likasalo la cipangano la Yehova wa makamu, wokhala pakati pa akerubi; ndipo ana awiriwo a Eli, Hofeni ndi Pinehasi anali komweko ndi likasa la cipangano la Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:4 nkhani