Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 30:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananena ndi Abyatara wansembeyo, mwana wa Ahimeleki, Unditengere kuno efodi. Abyatara nabwera ndi efodi kwa Davide.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:7 nkhani