Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 30:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anafika kuli anthu mazana awiri amene analema osakhoza kutsata Davide, amenenso anawakhalitsa kukamtsinje Besori; ndipo iwowa anaturuka kucingamira Davide, ndi amene anali naye; ndipo pakuyandikira Davide anawafunsa ngati ali bwanji.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:21 nkhani