Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 30:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananena naye, Kodi udzanditsogolera kufikira ku khamulo? Nati iye, Mundilumbirire kwa Mulungu, kuti simudzandipha, kapena kundipereka m'dzanja la mbuye wanga, ndipo ndidzatsika nanu kuli khamu limene.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30

Onani 1 Samueli 30:15 nkhani