Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 29:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akalonga a Afilisti ananyamuka ndi mazana ao ndi zikwi zao; ndipo Davide ndi anthu ace ananyamuka ndi a pambuyo pamodzi ndi Akisi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29

Onani 1 Samueli 29:2 nkhani