Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 29:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Tsono Afilisti anasonkhanitsa makamu ao onse ku Afeki; ndipo Aisrayeli anamanga ku citsime ca m'Jezreeli.

2. Ndipo akalonga a Afilisti ananyamuka ndi mazana ao ndi zikwi zao; ndipo Davide ndi anthu ace ananyamuka ndi a pambuyo pamodzi ndi Akisi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29