Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 28:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Sauli anafunsira kwa Yehova, Yehova sanamyankha ngakhale ndi maloto, kapena ndi Urimu, kapena ndi aneneri.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:6 nkhani