Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 28:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso Yehova adzapereka Israyeli pamodzi ndi iwe m'dzanja la Afilisti; ndipo mawa iwe ndi ana ako mudzakhala kuli ine; Yehova adzaperekanso khamu la Aisrayeli m'dzanja la Afilisti.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:19 nkhani