Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali munthu ku Maoni, amene katundu wace anali ku Karimeli; iyeyu anali womveka ndithu, anali nazo nkhosa zikwi zitatu, ndi mbuzi cikwi cimodzi; ndipo analikusenga nkhosa zace ku Karimeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:2 nkhani