Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anthu aja anaticitira zabwino ndithu, sanaticititsa manyazi, ndi panalibe kanthu kadatisowa, nthawi zonse tinali kuyenderana nao kubusa kuja;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:15 nkhani