Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa anthu ace, Munthu yense wa inu amangirire lupanga lace. Namangirira munthu yense lupanga lace; ndi Davide yemwe anamangirira lupanga lace; ndipo anakwera kumtsata Davide monga anthu mazana anai, koma mazana awiri anadika akatundu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:13 nkhani