Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 24:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Davide analetsa anyamata ace ndi mau awa, osawaloleza kuukira Sauli. Ndipo Sauli ananyamuka, naturuka m'phangamo, namuka njira yace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:7 nkhani