Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 24:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso atate wanga, penyani, inde penyani mkawo wa mwinjiro wanu m'dzanja langa; popeza ndinadula mkawo wa mwinjiro wanu, osakuphani, mudziwe, nimuone kuti mulibe coipa kapena kulakwa m'dzanja langa, ndipo sindinakucimwirani, cinkana inu musaka moyo wanga kuti muugwire,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:11 nkhani