Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono Davide anafunsiranso kwa Yehova. Ndipo Yehova anamyankha iye, nati, Nyamuka, nutsikire ku Keila; pakuti ndidzapereka Afilisti m'dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:4 nkhani