Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anamuka mbali yina ya phiri, Davide ndi anthu ace kutseri kwace; ndipo Davide anafulumira kuthawa, cifukwa ca kuopa Sauli; popeza Sauli ndi anthu ace anazinga Davide ndi anthu ace kwete kuti awagwire.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:26 nkhani