Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 22:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Doegi wa ku Edomu, anaimirira ndi anyamata a Sauli, nayankha, nati, Ine ndinamuona mwana wa Jeseyo alikufika ku Nobi, kwa Ahimeleki mwana wa Ahitubu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 22

Onani 1 Samueli 22:9 nkhani