Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 22:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero Davide anacoka kumeneko, napulumukira ku phanga la ku Adulamu; ndipo pamene abale ace ndi banja lonse la atate wace anamva, iwo anatsikira kumeneko kwa iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 22

Onani 1 Samueli 22:1 nkhani