Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo pocoka mnyamatayo, Davide anauka cakumwera, nagwa nkhope yace pansi, nawerama katatu; ndipo iwowa anapsompsonana, nalirirana, kufikira Davide analiritsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:41 nkhani