Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide analumbiranso nati, Atate wako adziwatu kuti wandikomera mtima; nati, Jonatani asadziwe ici, kuti angamve cisoni; koma pali Yehova, ndiponso pali moyo wako, pakati pa ine ndi imfa pali ngati phazilimodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:3 nkhani