Namyankha, Usatero iai, sudzafa; ona, atate, wanga sacita kanthu kakakuru kapena kakang'ono wosandidziwitsa ine; atate wanga adzandibisiranji cinthu cimeneci? Si kutero ai.