Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Sauli sananena kanthu tsiku lomwelo; cifukwa anaganizira, Kanthu kanamgwera iye, ali wodetsedwa; indedi ali wodetsedwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:26 nkhani