Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mfumu nikhala pa mpando wace, monga adafocita nthawi zina, pa mpando wa pafupi pa khoma. Ndipo Jonatani anaimirira, ndi Abineri anakhala pa mbali ya Sauli; koma Davide anasoweka pamalo pace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:25 nkhani