Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu alange Jonatani, ndi kuonjezapo, ngati atate wanga akondwera kukucitira coipa, ine osakuululira, ndi kukucotsa kuti upite mumtendere; ndipo Yehova akhale nawe, monga anakhala naye atate wanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:13 nkhani