Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jonatani anati kwa Davide, Yehova, Mulungu wa Israyeli, akhale mboni; nditaphera mwambi atate wanga mawa dzuwa lino, kapena mkuca, onani, pakakhala kanthu kabwino kakucitira Davide, sindidzakutumira mthenga ndi kukuululira kodi?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:12 nkhani