Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanga umaponnderezeranji nsembe yanga ndi copereka canga, zimene ndinalamulira m'mokhalamo mwanga; ndipo ucitira ana ako ulemu koposa Ine, kudzinenepetsa inu nokha ndi zokometsetsa za zopereka zao zonse za Aisrayeli, anthu anga?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:29 nkhani