Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi sindinasankhula iye pakati pa mafuko onse a Israyeli, akhale wansembe wanga, kuti apereke nsembe pa guwa langa, nafukize zonunkhira, nabvale efodi pamaso panga? Kodi sindinapatsa banja la kholo lako zopereka zonse za kumoto za ana a Israyeli?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:28 nkhani