Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eli anali wokalamba ndithu; namva zonse ana ace anacitira Aisrayeli onse, ndi kuti anagona ndi akazi akusonkhana pa khomo la cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:22 nkhani