Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nacipisa m'cimphuli, kapena mumkhate, kapena m'nkhali, kapena mumphika; yonse imene cobvuuliraco cinaiturutsa, wansembeyo anaitenga ikhale yace. Adafotero ku Silo ndi Aisrayeli onse akufika kumeneko.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:14 nkhani