Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo macitidwe a ansembe akucitira anthu ndiwo, kuti pamene munthu ali yense akapereka nsembe, mnyamata wa wansembeyo akabwera, nyama iri ciwirire, ndi cobvuulira ca ngowe ca mana atatu m'dzanja lace;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:13 nkhani