Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 19:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza iye anataya moyo wace nakantha Mfilistiyo, ndipo Yehova anacitira Aisrayeli onse cipulumutso cacikuru, inu munaciona, nimnnakondwera; tsono mudzacimwiranji mwazi wosalakwa, ndi kumupha Davide popanda cifukwa?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:5 nkhani