Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 19:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jonatani analankhula ndi atate wace mobvomereza Davide, nanena naye, Mfumu asacimwire mnyamata wace Davide; cifukwa iyeyo sanacimwira inu, ndipo nchito zace anakucitirani zinali zabwino ndithu;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:4 nkhani