Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 19:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anatumiza mithenga kuti igwire Davide, ndipo pamene inaona gulu la aneneri alikunenera, ndi Samueli mkuru wao alikuimapo, mzimu wa Mulungu unagwera-mithenga ya Sauli, ninenera iyonso.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:20 nkhani