Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:57 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Davide anabwera, atapha Mfilistiyo, Abineri anamtenga, nafika naye pamaso pa Sauli, mutu wa Mfilistiyo uli m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:57 nkhani