Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pamene Mfilistiyo anadzikonza, nadza, nasendera pafupi kuti akomane ndi Davide, Davide anafulumira, nathamangira ku khamulo, kuti akomane ndi Mfilistiyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:48 nkhani