Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine kapolo wanu ndinapha mkango ndi cimbalangondo zonse ziwiri; ndipo Mfilisti uyu wosadulidwa adzakhala ngati mmodzi wa izo, popeza wanyoza makamu a Mulungu wamoyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:36 nkhani