Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 16:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jese anatenga buru namsenza mkate, ndi thumba la vinyo, ndi: mwana wa mbuzi, nazitumiza kwa Sauli ndi Davide mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16

Onani 1 Samueli 16:20 nkhani