Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 15:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli sanadzanso kudzaona Sauli kufikira tsiku la imfa yace; koma Samueli analira cifukwa ca Sauli; ndipo Yehova anali ndi cisoni kuti anamlonga Sauli mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:35 nkhani