Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 15:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kundicititsa cisoni kuti ndinaika Sauli akhale mfumu; pakuti wabwerera wosanditsata Ine, ndipo sanacita malamulo anga, Ndipo Samueli anakwiya; nalira kwa Yehova usiku wonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 15

Onani 1 Samueli 15:11 nkhani