Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakati pa mipata imene Jonatani anafuna kupitapo kunka ku kaboma ka Afilisti, panali phiri lathanthwe pa mbali yina, ndi phiri lathanthwe pa mbali inzace; ndipo dzina la linalo ndilo Bozezi, ndi la linzace ndilo Sene.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:4 nkhani