Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti, pali Yehova wakupulumutsa Israyeli, cingakhale ciri m'mwana wanga Jonatani, koma adzafa ndithu. Koma pakati pa anthu onse panalibe mmodzi wakumyankha iye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:39 nkhani