Ndipo anthuwo anathamangira zowawanyazo, natenga nkhosa, ndi ng'ombe, ndi ana a ng'ombe, naziphera pansi; anthu nazidya ziri ndi mwazi wao.